1 Samueli 22:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo anawatenga kunka nao pamaso pa mfumu ya Mowabu; ndipo iwo anakhala naye nthawi yonse Davide anali ku lingalo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo anawatenga kunka nao pamaso pa mfumu ya Mowabu; ndipo iwo anakhala naye nthawi yonse Davide anali ku lingalo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Choncho adaŵasiya kumeneko makolo akewo kwa mfumu ya ku Mowabuko, ndipo iwo adakhala komweko nthaŵi yonse imene Davide ankabisala kuphanga kuja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Choncho iye anawasiya kwa mfumu ya Mowabu ndipo anakhala naye nthawi yonse imene Davide ankabisala ku phanga kuja. Onani mutuwo |