1 Samueli 22:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo mfumu inati, Ukufa ndithu Ahimeleki, iwe ndi banja lonse la atate wako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo mfumu inati, Ukufa ndithu Ahimeleki, iwe ndi banja lonse la atate wako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Komabe mfumu idati, “Iwe Ahimeleki, ndi onse a m'banja la bambo wako, mufa ndithu nonse!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Koma mfumu inati, “Iwe Ahimeleki ndi banja lonse la abambo ako mudzaphedwa ndithu.” Onani mutuwo |