1 Samueli 20:7 - Buku Lopatulika7 Tsono akati, Chabwino; kapolo wako adzakhala ndi mtendere; koma akapsa mtima, uzindikirepo kuti anatsimikiza mtima kundichitira choipa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Tsono akati, Chabwino; kapolo wako adzakhala ndi mtendere; koma akapsa mtima, uzindikirepo kuti anatsimikiza mtima kundichitira choipa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Akati, ‘Chabwino’, zinthu zidzandiyendera bwino, ine kapolo wako. Koma akakhala wokwiyabe, udziŵe kuti watsimikiza mtima kuti andichita choipa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Akanena kuti, ‘Wachita bwino,’ ndiye kuti zinthu zindiyendera bwino ine mtumiki wako. Koma ngati akapsa mtima, ndiye udziwe kuti iwo atsimikiza zondichita zoyipa. Onani mutuwo |