1 Samueli 20:6 - Buku Lopatulika6 Atate wako akandifuna pang'ono ponse, unene kuti, Davide anandiumirira ndimlole athamangire kwao ku Betelehemu, pakuti kumeneko kuli nsembe ya pachaka ya banja lao lonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Atate wako akandifuna pang'ono ponse, unene kuti, Davide anandiumirira ndimlole athamangire kwao ku Betelehemu, pakuti kumeneko kuli nsembe ya pachaka ya banja lao lonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Abambo ako akandifuna, uŵauze kuti, ‘Davide adandiwumiriza kuti ndimlole kuti athamangire ku mzinda wakwao ku Betelehemu. Akuti kumeneko kuli nsembe yapachaka ya banja lonse.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ngati abambo ako akafunsa za ine, ukawawuze kuti, ‘Davide anandiwumiriza kuti ndimulole apite msanga kwawo ku Betelehemu, chifukwa akupereka nsembe yapachaka ya banja lonse.’ Onani mutuwo |