Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 20:28 - Buku Lopatulika

28 Ndipo Yonatani anayankha Saulo, Davide anandiumiriza ndimlole amuke ku Betelehemu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 Ndipo Yonatani anayankha Saulo, Davide anandiumiriza ndimlole amuke ku Betelehemu;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Yonatani adayankha kuti, “Davide adandipempha mondiwumiriza kuti ndimlole apite ku Betelehemu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Yonatani anayankha kuti, “Davide anandiwumiriza kuti ndimulole kuti apite ku Betelehemu.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 20:28
3 Mawu Ofanana  

Ndipo kunali tsiku lachiwiri mwezi utakhala, Davide adasowekanso pamalo pake; ndipo Saulo anati kwa Yonatani mwana wake, Mwana wa Yese walekeranji kubwera kudya dzulo ndi lero lomwe?


nati, Ndiloleni, ndimuke; chifukwa banja lathu lipereka nsembe m'mzindamo; ndi mbale wanga anandiuzitsa ndifikeko; tsono ngati wandikomera mtima undilole ndichoke, ndikaone abale anga. Chifukwa cha ichi safika ku gome la mfumu.


Atate wako akandifuna pang'ono ponse, unene kuti, Davide anandiumirira ndimlole athamangire kwao ku Betelehemu, pakuti kumeneko kuli nsembe ya pachaka ya banja lao lonse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa