1 Samueli 2:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo iye ananena nao, Mumachitiranji chotere: popeza ndilinkumva za machitidwe anu oipa kwa anthu onsewa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo iye ananena nao, Mumachitiranji chotere: popeza ndilinkumva za machitidwe anu oipa kwa anthu onsewa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Tsono adafunsa ana akewo kuti, “Chifukwa chiyani mukuchita zinthu zotere? Ndilikumvatu kwa anthu zonse zoipa zimene mukuchita. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Choncho anawafunsa kuti, “Nʼchifukwa chiyani mukuchita zinthu zotere? Ine ndikumva kuchokera kwa anthu onse za zoyipa zanuzo. Onani mutuwo |