1 Samueli 19:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo wina anauza Saulo, kuti, Onani Davide ali ku Nayoti mu Rama. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo wina anauza Saulo, kuti, Onani Davide ali ku Nayoti m'Rama. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Saulo atamva kuti Davide ali ku Nayoti ku Rama, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Sauli anamva kuti, “Davide ali ku Nayoti ku Rama.” Onani mutuwo |