1 Samueli 18:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo kuyambira tsiku lomwelo ndi m'tsogolo mwake, Saulo anakhala maso pa Davide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo kuyambira tsiku lomwelo ndi m'tsogolo mwake, Saulo anakhala maso pa Davide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Motero Saulo ankamuwona ndi diso loipa Davide kuyambira tsiku limenelo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ndipo kuyambira tsiku limeneli Sauli ankamuchitira nsanje Davide. Onani mutuwo |