Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 17:56 - Buku Lopatulika

56 Ndipo mfumu inati, Ufunsire kuti mnyamatayo ndi mwana wa yani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

56 Ndipo mfumu inati, Ufunsire kuti mnyamatayo ndi mwana wa yani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

56 Apo mfumu idati, “Kafunse kuti kodi mnyamata ameneyu ndi mwana wa yani?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

56 Mfumu inati, “Pita kafufuze kuti mnyamata ameneyu ndi mwana wa yani.”

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 17:56
3 Mawu Ofanana  

Ndipo Saulo anati kwa Davide, Sukhoza iwe kukomana ndi Mfilisti uyu kukaponyana naye; pakuti iwe ndiwe mnyamata, koma iye anazolowera nkhondo kuyambira ubwana wake.


Ndipo pamene Saulo anaona Davide alikutulukira kwa Mfilistiyo, iye anati kwa Abinere, kazembe wa khamu la nkhondo, Abinere, mnyamata uyu ndi mwana wa yani? Nati Abinere, Pali moyo wanu, mfumu, ngati ndidziwa.


Ndipo pamene Davide anabwera, atapha Mfilistiyo, Abinere anamtenga, nafika naye pamaso pa Saulo, mutu wa Mfilistiyo uli m'dzanja lake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa