1 Samueli 17:53 - Buku Lopatulika53 Ndipo ana a Israele atathamangira Afilisti, anabwerera nafunkha za m'zithando zao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201453 Ndipo ana a Israele atathamangira Afilisti, anabwerera nafunkha za m'zithando zao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa53 Ndipo Aisraele adabwererako kumene ankapirikitsa Afilisti kuja, nadzafunkha m'zithando zankhondo za Afilistiwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero53 Aisraeli anabwerako kothamangitsa Afilisti kuja ndipo anadzatenga zonse zimene zinali mʼmisasa ya Afilistiwo. Onani mutuwo |