1 Samueli 17:38 - Buku Lopatulika38 Ndipo Saulo anaveka Davide zovala zake za iye yekha, namveka chisoti chamkuwa pamutu pake, namvekanso malaya aunyolo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ndipo Saulo anaveka Davide zovala zake za iye yekha, namveka chisoti chamkuwa pamutu pake, namvekanso malaya aunyolo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Tsono Saulo adaveka Davide zovala zake zankhondo. Adamveka chisoti chamkuŵa ndi malaya achitsulo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Ndipo Sauli anamveka Davide mwinjiro wake. Anamuveka zovala zankhondo ndi chipewa cha mkuwa. Onani mutuwo |