1 Samueli 17:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo anthuwo anamyankha motero, nati, Adzamchitira munthu wakumupha iye mwakutimwakuti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo anthuwo anamyankha motero, nati, Adzamchitira munthu wakumupha iye mwakutimwakuti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Anthu adamuuzanso zomwe zija zimene mfumu idaati idzachitire munthu wodzapha Goliyatiyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Anthu anamuwuzanso zonse zimene mfumu inanena kuti idzachitira munthu amene adzapha Mfilisitiyo. Onani mutuwo |