1 Samueli 17:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo Aisraele onse, pakumuona munthuyo, anamthawa, naopa kwambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo Aisraele onse, pakumuona munthuyo, anamthawa, naopa kwambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Aisraele onse atamuwona munthuyo, adathaŵa chifukwa ankamuwopa kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Aisraeli ataona munthuyo, anamuthawa ndi mantha aakulu. Onani mutuwo |