1 Samueli 17:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo Davide anasiya akatundu ake m'dzanja la wosungira akatundu, nathamangira ku khamulo, nadza nawalonjera abale ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo Davide anasiya akatundu ake m'dzanja la wosungira akatundu, nathamangira ku khamulo, nadza nawalonjera abale ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Tsono zakudya zija Davide atasiyira munthu wosunga katundu, adathamangira kumene kunali ankhondo, nakalonjera abale ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Tsono Davide anasiyira zakudya zija munthu wosunga katundu nathamangira kumene kunali ankhondo kuja ndi kukalonjera abale ake. Onani mutuwo |