1 Samueli 17:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo Israele ndi Afilisti anandandalitsa nkhondo zao, khamu lina kuyang'anana ndi khamu lina. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo Israele ndi Afilisti anandandalitsa nkhondo zao, khamu lina kuyang'anana ndi khamu lina. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Aisraele ndi Afilisti adaandanda pa mzere wankhondo moyang'anana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Aisraeli ndi Afilisti anandanda pa mzere wankhondo moyangʼanana. Onani mutuwo |