1 Samueli 16:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Samuele anati, Ndikamuka bwanji? Saulo akachimva, adzandipha. Ndipo Yehova anati, Umuke nayo ng'ombe yaikazi, nunene kuti, Ndadza kudzaphera nsembe kwa Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Samuele anati, Ndikamuka bwanji? Saulo akachimva, adzandipha. Ndipo Yehova anati, Umuke nayo ng'ombe yaikazi, nunene kuti, Ndadza kudzaphera nsembe kwa Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Samuele adafunsa Chauta kuti, “Kodi ndingathe bwanji kupitako? Saulo akamva zimenezi, adzandipha.” Chauta adati, “Utenge ng'ombe yaikazi popita, ndipo ukanene kuti, ‘Ndadzapereka nsembe kwa Chauta.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Koma Samueli anati, “Kodi ndingapite bwanji? Sauli akamva zimenezi adzandipha.” Yehova anayankha, “Tenga ngʼombe yayikazi ndipo ukanene kuti, ‘Ndabwera kudzapereka nsembe kwa Yehova. Onani mutuwo |