1 Samueli 16:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo anatumiza munthu, nabwera naye. Tsono iye anali wofiirira, ndi wa nkhope yokongola, ndi maonekedwe okoma. Ndipo Yehova anati, Nyamuka umdzoze, pakuti ndi ameneyu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo anatumiza munthu, nabwera naye. Tsono iye anali wofiirira, ndi wa nkhope yokongola, ndi maonekedwe okoma. Ndipo Yehova anati, Nyamuka umdzoze, pakuti ndi ameneyu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Choncho adatuma munthu kukamtenga, ndipo adabwera naye. Anali wofiirira ndi wa maonekedwe okongola ochititsa kaso. Pamenepo Chauta adati, “Ndi ameneyu, mdzoze.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Choncho anatuma munthu kukamutenga ndipo anabwera naye. Iye anali wofiirira, wa maonekedwe abwino ochititsa kaso. Ndipo Yehova anati, “Mudzoze popeza ndi ameneyu.” Onani mutuwo |