Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 15:31 - Buku Lopatulika

31 Chomwecho Samuele anabwerera natsata Saulo; ndi Saulo analambira Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

31 Chomwecho Samuele anabwerera natsata Saulo; ndi Saulo analambira Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

31 Choncho Samuele adabwereradi, natsagana ndi Saulo. Ndipo Sauloyo adapembedza Chauta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

31 Pamenepo Samueli anabwerera ndi Sauli, ndipo Sauli anapembedza Yehova.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 15:31
4 Mawu Ofanana  

Pamenepo Davide ananyamuka pansi, nasamba, nadzola, nasintha zovala; nafika kunyumba ya Yehova, napembedza; pamenepo anafika kunyumba yake; ndipo powauza anamuikira chakudya, nadya iye.


Ndipo Samuele ananena ndi Saulo, Ine sindibwerera nanu; pakuti munakaniza mau a Yehova, ndipo Yehova anakaniza inu, kuti simudzakhalanso mfumu ya Israele.


Pomwepo iye anati, Ndinachimwa, koma mundichitire ulemu tsopano pamaso pa akulu a anthu anga, ndi pamaso pa Israele, nimubwerere pamodzi ndi ine, kuti ndikalambire Yehova Mulungu wanu.


Ndipo Samuele anati, Bwerani naye kwa ine kuno Agagi mfumu ya Aamaleke. Ndipo Agagi anabwera kwa iye mokondwera. Nati Agagi, Zoonadi kuwawa kwa imfa kunapitirira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa