1 Samueli 15:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo pakupotoloka Samuele kuti achoke, iye anagwira chilezi cha mwinjiro wake, ndipo chinang'ambika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo pakupotoloka Samuele kuti achoke, iye anagwira chilezi cha mwinjiro wake, ndipo chinang'ambika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Pamene Samuele ankatembenuka kuti azipita, Saulo adagwira mpendero wa mkanjo wake, ndipo mkanjowo udang'ambika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Samueli akutembenuka kuti azipita, Sauli anagwira mpendero wa mkanjo wake, ndipo unangʼambika. Onani mutuwo |