1 Samueli 15:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Samuele ananena ndi Saulo, Yehova ananditumiza ine kukudzozani mukhale mfumu ya anthu ake Aisraele; chifukwa chake tsono mumvere kunena kwa mau a Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Samuele ananena ndi Saulo, Yehova ananditumiza ine kukudzozani mukhale mfumu ya anthu ake Aisraele; chifukwa chake tsono mumvere kunena kwa mau a Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tsiku lina Samuele adauza Saulo kuti, “Paja Chauta adaatuma ine kuti ndikudzozeni, kuti mukhale mfumu ya anthu ake Aisraele. Nchifukwa chake tsono imvani uthenga wochokera kwa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Samueli anawuza Sauli kuti, “Yehova anandituma ine kuti ndikudzozeni kukhala mfumu ya anthu ake, Aisraeli. Tsopano imvani zimene Yehova akunena. Onani mutuwo |