Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 14:42 - Buku Lopatulika

42 Ndipo Saulo anati, Muchite maere pakati pa ine ndi Yonatani mwana wanga. Ndipo anagwera Yonatani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

42 Ndipo Saulo anati, Muchite maere pakati pa ine ndi Yonatani mwana wanga. Ndipo anagwera Yonatani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

42 Tsono Saulo adati, “Chitani maere pakati pa ine ndi mwana wanga Yonatani.” Ndipo maere adagwera Yonatani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

42 Sauli anati, “Chitani maere pakati pa ine ndi Yonatani mwana wanga.” Ndipo maere anagwera Yonatani.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 14:42
6 Mawu Ofanana  

Maere aponyedwa pamfunga; koma ndiye Yehova alongosola zonse.


Maere aletsa makangano, nulekanitsa amphamvu.


Ndipo anati yense kwa mnzake, Tiyeni tichite maere, kuti tidziwe choipa ichi chatigwera chifukwa cha yani. M'mwemo anachita maere, ndipo maere anagwera Yona.


nayandikizitsa a m'nyumba yake mmodzimmodzi; ndipo Akani, mwana wa Karimi, mwanu wa Zabidi, mwana wa Zera, wa fuko la Yuda anagwidwa.


Chifukwa chake Saulo ananena ndi Yehova, Mulungu wa Israele, muonetse choonadi. Ndipo maere anagwera Saulo ndi Yonatani; koma anthuwo anapulumuka.


Pamenepo Saulo ananena ndi Yonatani, Undiuze chimene unachita. Ndipo Yonatani anamuuza, nati, Zoonadi ndinangolawako uchi pang'ono ndi nsonga ya ndodo inali m'dzanja langa: ndipo onani ndiyenera kufa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa