1 Samueli 14:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo anakantha Afilisti tsiku lija kuyambira ku Mikimasi kufikira ku Ayaloni, ndipo anthu anafooka kwambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo anakantha Afilisti tsiku lija kuyambira ku Mikimasi kufikira ku Ayaloni, ndipo anthu anafooka kwambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Tsikulo Aisraele adapha Afilisti kuyambira ku Mikimasi mpaka ku Ayaloni. Koma Aisraelewo anali pafupi kukomoka nayo njala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Tsiku limenelo Aisraeli anapha Afilisti kuchokera ku Mikimasi mpaka ku Ayaloni. Koma Aisraeliwo analefuka kwambiri ndi njala. Onani mutuwo |