1 Samueli 14:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo kunali m'mene Saulo anali chilankhulire ndi wansembeyo, phokoso la m'chigono cha Afilisti linachitikabe, nilikula; ndipo Saulo ananena ndi wansembeyo, Bweza dzanja lako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo kunali m'mene Saulo anali chilankhulire ndi wansembeyo, phokoso la m'chigono cha Afilisti linachitikabe, nilikula; ndipo Saulo ananena ndi wansembeyo, Bweza dzanja lako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Pamene Saulo ankalankhula ndi wansembeyo, phokoso linkakulirakulira ku zithando za Afilisti. Tsono Saulo adauza wansembe uja kuti, “Leka, usaombeze!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Pamene Sauli amayankhula ndi wansembe, phokoso limanka likulirakulira mu msasa wa Afilisti, Kotero Sauli anati kwa wansembe, “Leka kuwombeza.” Onani mutuwo |