1 Samueli 13:12 - Buku Lopatulika12 chifukwa chake ndinati, Afilisti adzatitsikira pano pa Giligala, ndisanapembedze Yehova; potero ndinadzifulumiza, ndi kupereka nsembe yopsereza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 chifukwa chake ndinati, Afilisti adzatitsikira pano pa Giligala, ndisanapembedze Yehova; potero ndinadzifulumira, ndi kupereka nsembe yopsereza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 ndinati, ‘Tsopano Afilisti abwera kudzandithira nkhondo ku Giligala kuno, ine ndisanapemphe Chauta kuti andikomere mtima.’ Motero ndinadzikakamiza kupereka nsembe yopserezayi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 ndinati, ‘Tsopano Afilisti abwera kudzandithira nkhondo ku Giligala kuno, chonsecho sindinapemphe Yehova kuti andikomere mtima.’ Motero ndinakakamizika kupereka nsembe yopsereza.” Onani mutuwo |