1 Samueli 12:22 - Buku Lopatulika22 Pakuti Yehova sadzasiya anthu ake chifukwa cha dzina lake lalikulu; pakuti kudamkomera Yehova kukuyesani inu anthu a Iye yekha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Pakuti Yehova sadzasiya anthu ake chifukwa cha dzina lake lalikulu; pakuti kudamkomera Yehova kukuyesani inu anthu a Iye yekha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Chauta sadzataya anthu ake, kuti dzina lake lalikulu linganyozeke, poti chidamukondweretsa kuti akusandutseni anthu ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Yehova adzakana anthu ake kuopa kuti dzina lake lamphamvu linganyozeke, pakuti chinamukondweretsa Yehova kuti akusandutseni inu kukhala anthu ake. Onani mutuwo |