1 Samueli 12:21 - Buku Lopatulika21 musapatukire inu kutsata zinthu zachabe, zosapindulitsa, zosapulumutsa, popeza zili zopanda pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 musapatukire inu kutsata zinthu zachabe, zosapindulitsa, zosapulumutsa, popeza zili zopanda pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Ndipo musatsate mafano achabe amene alibe phindu, amene sangathe kupulumutsa poti ngopandapake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Ndipo musatsate mafano achabechabe amene alibe phindu ndipo sangakupulumutseni popeza ndi achabechabe. Onani mutuwo |