1 Samueli 11:10 - Buku Lopatulika10 Chifukwa chake anthu a ku Yabesi anati, Mawa tidzatulukira kwa inu, ndipo mudzatichitira chokomera inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Chifukwa chake anthu a ku Yabesi anati, Mawa tidzatulukira kwa inu, ndipo mudzatichitira chokomera inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Nchifukwa chake adauza Nahasi kuti, “Maŵa tidzadzipereka kwa inu, ndipo mutichite chilichonse chimene chikukomereni.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Choncho anthu a ku Yabesi anawuza Nahasi kuti, “Mawa tidzadzipereka kwa inu ndipo inu mudzachite nafe chilichonse chokukomerani.” Onani mutuwo |