1 Samueli 10:20 - Buku Lopatulika20 Chomwecho Samuele anayandikizitsa mafuko onse a Israele, ndipo fuko la Benjamini linasankhidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Chomwecho Samuele anayandikizitsa mafuko onse a Israele, ndipo fuko la Benjamini linasankhidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Choncho Samuele adasonkhanitsa mafuko onse a Aisraele, ndipo pochita maere, fuko la Benjamini ndilo lidasankhidwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Samueli atasonkhanitsa mafuko onse a Israeli, fuko la Benjamini linasankhidwa. Onani mutuwo |