1 Samueli 10:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo mbale wa atate wa Saulo anati, Undiuze chimene Samuele analankhula nawe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo mbale wa atate wa Saulo anati, Undiuze chimene Samuele analankhula nawe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Apo mbale wa bambo wakeyo adati, “Ndikukupempha, uzeko zimene adanena Samuele.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Amalume ake a Sauli anati, “Chonde, ndifotokozereniko zimene Samueli wakuwuzani.” Onani mutuwo |