1 Samueli 10:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo pamene adatha kunenera anafika kumsanjeko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo pamene adatha kunenera anafika kumsanjeko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Atatha kulosako, Saulo adapita ku kachisi ku phiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Sauli atasiya kuloserako, anapita ku kachisi ku phiri. Onani mutuwo |