1 Samueli 1:28 - Buku Lopatulika28 chifukwa chake inenso ndinampereka kwa Yehova; masiku onse a moyo wake aperekedwa kwa Yehova. Ndipo analambira Yehova pomwepo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 chifukwa chake inenso ndinampereka kwa Yehova; masiku onse a moyo wake aperekedwa kwa Yehova. Ndipo analambira Yehova pomwepo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Nchifukwa chake ndampereka kwa Chauta. Moyo wake wonse mwanayu adzakhala wake wa Chauta.” Ndipo onsewo adapembedza Chauta kumeneko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Ndiye tsopano ine ndikumupereka kwa Yehova. Pa moyo wake wonse adzakhala wa Yehova.” Ndipo onse anapembedza Yehova kumeneko. Onani mutuwo |