1 Samueli 1:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo iwo anauka mamawa, nalambira pamaso pa Yehova, nabwerera, nafikanso kwao ku Rama; ndipo Elikana anadziwa mkazi wake Hana, Yehova namkumbukira iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo iwo anauka mamawa, nalambira pamaso pa Yehova, nabwerera, nafikanso kwao ku Rama; ndipo Elikana anadziwa mkazi wake Hana, Yehova namkumbukira iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 M'maŵa mwake Elikana ndi banja lake adadzuka m'mamaŵa, ndipo atatha kupembedza Chauta, adabwerera kwao ku Rama. Elikana adakhala ndi mkazi wake Hana, ndipo Chauta adamkumbuka Hanayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Elikana ndi banja lake anadzuka mmawa mwake nakapemphera pamaso pa Yehova. Pambuyo pake anabwerera kwawo ku Rama. Elikana anakhala pamodzi ndi mkazi wake, ndipo Yehova anamukumbuka Hanayo. Onani mutuwo |