1 Samueli 1:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo iye anati, Mumkomere mtima mdzakazi wanu. Chomwecho mkaziyo anamuka, nakadya, ndi nkhope yake siinakhalanso yachisoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo iye anati, Mumkomere mtima mdzakazi wanu. Chomwecho mkaziyo anamuka, nakadya, ndi nkhope yake siinakhalanso yachisoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Tsono Hana adati, “Mundikomerebe mtima mdzakazi wanune.” Pompo mkaziyo adachoka nakadya, ndipo sadaonekenso wachisoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Hana anati, “Mundikomerebe mtima mtumiki wanune.” Kenaka anachoka nakadya, ndipo sanaonekenso wachisoni. Onani mutuwo |