Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Mbiri 5:3 - Buku Lopatulika

3 ana a Rubeni mwana woyamba wa Israele: Hanoki, ndi Palu, Hezironi, ndi Karimi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 ana a Rubeni mwana woyamba wa Israele: Hanoki, ndi Palu, Hezironi, ndi Karimi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Tsono ana a Rubeni naŵa: Hanoki, Palu, Hezironi ndi Karimi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 ana a Rubeni mwana woyamba wa Israeli ndi awa: Hanoki, Palu, Hezironi, ndi Karimi.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 5:3
3 Mawu Ofanana  

Ndi ana aamuna a Rubeni: Hanoki, ndi Palu, ndi Hezironi, ndi Karimi.


Akulu a mbumba za makolo ao ndi awa: ana aamuna a Rubeni, woyamba wa Israele ndiwo: Hanoki ndi Palu, Hezironi, ndi Karimi; amenewo ndiwo mabanja a Rubeni.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa