Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Mbiri 13:3 - Buku Lopatulika

3 ndipo tibwere nalo kwa ife likasa la Mulungu wathu, pakuti sitinafunako masiku a Saulo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 ndipo tibwere nalo kwa ife likasa la Mulungu wathu, pakuti sitinafunako masiku a Saulo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Tsono tibwere nalonso bokosi lachipangano la Chauta wathu. Paja pa nthaŵi ya Saulo sitidalisamale Bokosilo.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Tiyeni tibweretsenso Bokosi la Mulungu wathu kuno kwathu, pakuti nthawi ya Sauli sitinafunse za bokosili.”

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 13:3
11 Mawu Ofanana  

Ndipo Davide anati kwa msonkhano wonse wa Israele, Chikakomera inu, ndipo chikachokera kwa Yehova Mulungu wathu, titumize konse kuti abale athu otsala m'dziko lonse la Israele, ndi ansembe ndi Alevi okhala nao m'mizinda yao yokhala napo podyetsa, kuti asonkhane kwa ife;


Ndipo a msonkhano onse anati kuti adzachita; pakuti chidayenera chinthuchi pamaso pa anthu onse.


Pakuti, chifukwa cha kusalinyamula inu poyamba paja, Yehova Mulungu wathu anachita chotipasula, popeza sitinamfunafuna Iye monga mwa chiweruzo.


Taonani, tinachimva mu Efurata; tinachipeza kuchidikha cha kunkhalango.


Ndipo Saulo ananena ndi Ahiya, Bwera nalo likasa la Mulungu kuno. Pakuti likasa la Mulungu linali kumeneko masiku aja ndi ana a Israele.


Ndipo Saulo anati, Tiyeni titsikire usiku kwa Afilistiwo, ndi kuwawawanya kufikira kutayera, tisasiye munthu mmodzi wa iwowa. Ndipo iwo anati, Chitani chilichonse chikukomerani. Pamenepo wansembeyo anati, Tisendere kwa Mulungu kuno.


Ndipo iye anamfunsira kwa Yehova, nampatsa chakudya, nampatsanso lupanga la Goliyati Mfilistiyo.


Kodi ndayamba lero kumfunsira kwa Mulungu? Musatero iai; mfumu asanenera mnyamata wake kanthu, kapena nyumba yonse ya atate wanga; popeza ine mnyamata wanu sindidziwa kanthu ka izi zonse, ndi pang'ono ponse.


Chifukwa chake Davide anafunsira kwa Yehova, nati, Ndimuke kodi kukakantha Afilisti aja? Ndipo Yehova anati kwa Davide, Muka, nukanthe Afilisti, ndi kupulumutsa Keila.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa