Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 13:4 - Buku Lopatulika

4 Ndipo a msonkhano onse anati kuti adzachita; pakuti chidayenera chinthuchi pamaso pa anthu onse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndipo a msonkhano onse anati kuti adzachita; pakuti chidayenera chinthuchi pamaso pa anthu onse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Msonkhano wonse udavomereza zimenezo, poti anthu onse adaaona kuti nzabwino.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Gulu lonse linavomereza izi, pakuti anthu onse anaona kuti kunali kofunika kutero.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 13:4
6 Mawu Ofanana  

Ndipo anthu onse anachisamalira, ndipo chinawakomera; zilizonse adazichita mfumu zidakomera anthu onse.


ndipo tibwere nalo kwa ife likasa la Mulungu wathu, pakuti sitinafunako masiku a Saulo.


M'mwemo Davide anamemeza Aisraele onse kuyambira Sihori wa ku Ejipito mpaka polowera ku Hamati, kutenga likasa la Mulungu ku Kiriyati-Yearimu.


Ndipo chinthuchi chinayenera m'maso mwa mfumu ndi msonkhano wonse.


Nati, Chikakomera mfumu, ndipo ngati yandikomera mtima, ndi kumuyenera mfumu, ngatinso ndimchititsa kaso, alembe makalata kusintha mau a chiwembu cha Hamani mwana wa Hamedata wa ku Agagi, amene adawalembera kuononga Ayuda okhala m'maiko onse a mfumu;


Ndipo Mikala mwana wamkazi wa Saulo anakonda Davide; ndipo pakumva Saulo, anakondwera nako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa