Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Mbiri 1:9 - Buku Lopatulika

9 Ndi ana a Kusi: Seba, ndi Havila, ndi Sabita, ndi Raama, ndi Sabiteka. Ndi ana a Raama: Sheba, ndi Dedani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndi ana a Kusi: Seba, ndi Havila, ndi Sabita, ndi Raama, ndi Sabiteka. Ndi ana a Raama: Sheba, ndi Dedani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Ana a Kusi naŵa: Seba, Havila, Sabita, Raama ndi Sabiteka. Ana a Raama naŵa: Sheba ndi Dedani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Ana aamuna a Kusi anali: Seba, Havila, Sabita, Raama ndi Sabiteka Ana aamuna a Raama anali: Seba ndi Dedani.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 1:9
6 Mawu Ofanana  

Ndi ana aamuna a Kusi: Seba, ndi Havila, ndi Sabita, ndi Raama, ndi Sabiteka; ndi ana a Raama: Sheba ndi Dedani.


Ndi Kusi anabala Nimirodi; iye anayamba kukhala wamphamvu padziko.


Ana a Hamu: Kusi, ndi Ejipito, Puti, ndi Kanani.


Katundu wa pa Arabiya. M'nkhalango ya mu Arabiya mudzagona, inu makamu oyendayenda a Dedani.


Anthu a ku Dedani anakutsatsa malonda, zisumbu zambiri zinazolowerana nawe malonda ako, anabwera nazo minyanga ndi phingo kugulana nawe malonda.


Amalonda a ku Sheba ndi a ku Raama anagulana nawe malonda; anagula malonda ako ndi zonunkhira zoposa zilizonse, ndi miyala iliyonse ya mtengo wake, ndi golide.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa