1 Mbiri 1:10 - Buku Lopatulika10 Ndi Kusi anabala Nimirodi; iye anayamba kukhala wamphamvu padziko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndi Kusi anabala Nimirodi; iye anayamba kukhala wamphamvu pa dziko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Kusi adabereka Nimirodi. Iyeyu ndiye adayamba kukhala munthu wamphamvu pa dziko lonse lapansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Kusi anali abambo a Nimurodi amene anali wankhondo wamphamvu kwambiri pa dziko lapansi. Onani mutuwo |