1 Akorinto 9:11 - Buku Lopatulika11 Ngati takufeserani inu zauzimu, kodi nchachikulu ngati ife tituta za thupi lanu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ngati takufeserani inu zauzimu, kodi nchachikulu ngati ife tituta za thupi lanu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Ngati ife tidafesa zabwino zauzimu pakati panu, nanga tilekerenji kulandira kwa inu zotisoŵa m'moyo wathu wathupi? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ngati tidzala mbewu yauzimu pakati panu, kodi ndi chovuta kwambiri kuti tikolole zosowa zathu kuchokera kwa inu? Onani mutuwo |