1 Akorinto 8:11 - Buku Lopatulika11 Pakuti mwa chidziwitso chako wofookayo atayika, ndiye mbale amene Khristu anamfera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Pakuti mwa chidziwitso chako wofookayo atayika, ndiye mbale amene Khristu anamfera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Motero amene chikhulupiriro chake nchosalimba kwenikweni, adzatayika chifukwa cha iwe amene uli wodziŵa. Chonsecho tsono iyeyo ndi mbale wako amene Khristu adamufera! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Kotero kuti chifukwa cha chidziwitso chanu mʼbale wofowokayu amene chifukwa cha iye, Khristu anafa, wawonongeka chifukwa cha chidziwitso chanu. Onani mutuwo |