1 Akorinto 7:8 - Buku Lopatulika8 Koma ndinena kwa osakwatira, ndi kwa akazi amasiye, kuti kuli bwino kwa iwo ngati akhala monganso ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Koma ndinena kwa osakwatira, ndi kwa akazi amasiye, kuti kuli bwino kwa iwo ngati akhala monganso ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Kwa amene sali pa banja, ndiponso kwa azimai amasiye, mau anga ndi aŵa: Nkwabwino kuti iwo akhalebe paokha choncho ngati ineyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Tsono kwa osakwatira onse, ndi akazi amasiye ndikuti, ndi bwino kwa iwo kukhala osakwatira monga mmene ndilili inemu. Onani mutuwo |