1 Akorinto 7:21 - Buku Lopatulika21 Kodi unaitanidwa uli kapolo? Usasamalako; koma ngati ukhozanso kukhala mfulu, chita nako ndiko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Kodi unaitanidwa uli kapolo? Usasamalako; koma ngati ukhozanso kukhala mfulu, chita nako ndiko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Kodi unali kapolo pamene Mulungu adakuitana? Usavutike nazo. Komanso ngati upeza mwai woti ulandire ufulu, uugwiritse ntchito mwaiwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Kodi munali kapolo pamene Mulungu anakuyitanani? Musavutike nazo zimenezi. Koma ngati mutapeza mwayi woti mulandire ufulu, ugwiritseni ntchito mwayiwo. Onani mutuwo |