1 Akorinto 7:19 - Buku Lopatulika19 Mdulidwe ulibe kanthu, ndi kusadulidwa kulibe kanthu, koma kusunga kwa malamulo a Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Mdulidwe ulibe kanthu, ndi kusadulidwa kulibe kanthu, koma kusunga kwa malamulo a Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Kuumbala si kanthu ai, kusaumbala si kanthunso. Kanthu nkutsata malamulo a Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Mdulidwe si kanthu, kusachita mdulidwe si kanthunso. Chofunika nʼkusunga malamulo a Mulungu. Onani mutuwo |