1 Akorinto 7:10 - Buku Lopatulika10 Koma okwatitsidwawo ndiwalamulira, si ine ai, koma Ambuye, kuti mkazi asasiye mwamuna, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Koma okwatitsidwawo ndiwalamulira, si ine ai, koma Ambuye, kuti mkazi asasiye mwamuna, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Kwa anthu am'banja lamulo langa, limenetu kwenikweni ndi lochokera kwa Ambuye, ndi ili: Mkazi asalekane ndi mwamuna wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Kwa amene ali pa banja ndikupatsani lamulo ili (osati langa koma la Ambuye): Mkazi asalekane ndi mwamuna wake. Onani mutuwo |