1 Akorinto 6:4 - Buku Lopatulika4 Chifukwa chake, ngati muli nayo milandu ya zinthu za moyo uno, kodi muweruzitsa iwo amene ayesedwa achabe mu Mpingo? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Chifukwa chake, ngati muli nayo milandu ya zinthu za moyo uno, kodi muweruzitsa iwo amene ayesedwa achabe mu Mpingo? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono ngati muli ndi milandu pa zinthu zotere, bwanji mumaika anthu amene mpingo suŵayesa kanthu kuti aiweruze? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Nʼchifukwa chake, ngati pali milandu pa zinthu zotere, sankhani anthu ena kuti akhale oweruza ngakhale alibe udindo mu mpingo. Onani mutuwo |