1 Akorinto 6:3 - Buku Lopatulika3 Kodi simudziwa kuti tidzaweruza angelo? Koposa kotani nanga zinthu za moyo uno? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Kodi simudziwa kuti tidzaweruza angelo? Koposa kotani nanga zinthu za moyo uno? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Kodi simukudziŵa kuti tidzaweruza angelo? Nanji zinthu za moyo wapansipano? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Kodi simukudziwa kuti mudzaweruza angelo? Nanga bwanji zinthu za mʼmoyo uno! Onani mutuwo |