1 Akorinto 5:3 - Buku Lopatulika3 Pakuti inedi, thupi langa kulibe, koma mzimu wanga ulipo, ndaweruza kale, monga ngati ndilipo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pakuti inedi, thupi langa kulibe, koma mzimu wanga ulipo, ndaweruza kale, monga ngati ndilipo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Kunena za ine, ngakhale sindili nanu pamodzi, komabe mtima wanga uli nanu ndithu. Mwakuti ndamuweruza kale munthu amene adachita zimeneziyo, monga ngati ndili nanu pamodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ngakhale sindili nanu mʼthupi, ndili nanu mu mzimu. Ndipo ineyo ndapereka kale chiweruzo pa munthu amene amachita zotere, ngati kuti ndili komweko. Onani mutuwo |