1 Akorinto 5:12 - Buku Lopatulika12 Pakuti nditani nao akunja kukaweruza iwo? Kodi amene ali m'katimo simuwaweruze ndi inu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Pakuti nditani nao akunja kukaweruza iwo? Kodi amene ali m'katimo simuwaweruza ndi inu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Nanga kuweruza anthu amene adakali kunja, ndi ntchito yanga ngati? Si koma amene ali mu mpingo ndiwo muyenera kuŵaweruza? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Kodi ndipindulanji kuti ndiweruze anthu amene si a mu mpingo? Kodi simuyenera kuweruza iwo amene ali mu mpingo? Onani mutuwo |