1 Akorinto 4:2 - Buku Lopatulika2 Komatu pano pafunika za adindo, kuti munthu akhale wokhulupirika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Komatu pano pafunika za adindo, kuti munthu akhale wokhulupirika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Chofunika chachikulu pa akapitao otere nchakuti akhale okhulupirika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Chofunika kwambiri nʼchakuti amene apatsidwa udindo oyangʼanira aonetse kukhulupirika. Onani mutuwo |