1 Akorinto 4:18 - Buku Lopatulika18 Koma ena adzitukumula, monga ngati sindinalinkudza kwa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Koma ena adzitukumula, monga ngati sindinalinkudza kwa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ena mwayamba kudzitukumula, monga ngati sindidzabwerako kwanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ena mwa inu mukudzitukumula, ngati kuti sindingabwere kwanu. Onani mutuwo |